-
2 Samueli 17:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Ndiyeno ndibweretsa anthu onse kwa inu. Zimene zingachitikire munthu amene mukumusakasakayu, ndi zomwe zingachititse kuti anthu onse abwerere. Kenako anthu onse adzakhala mwamtendere.”
-