2 Samueli 17:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Komabe Abisalomu anati: “Tumani munthu akaitane Husai+ mbadwa ya Areki kuti timvenso maganizo ake.”
5 Komabe Abisalomu anati: “Tumani munthu akaitane Husai+ mbadwa ya Areki kuti timvenso maganizo ake.”