-
2 Samueli 17:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Choncho Husai anabwera kwa Abisalomu. Ndiyeno Abisalomu anamuuza kuti: “Ahitofeli wapereka malangizo amenewa. Kodi tichite zimene wanenazi? Ngati ayi, iweyo tiuze zochita.”
-