2 Samueli 17:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Panopa akubisala mʼphanga kapena mʼmalo ena.+ Ngati iwowo angakhale oyamba kuukira gulu lanu, nkhani idzafala kuti, ‘Anthu amene akutsatira Abisalomu agonjetsedwa.’
9 Panopa akubisala mʼphanga kapena mʼmalo ena.+ Ngati iwowo angakhale oyamba kuukira gulu lanu, nkhani idzafala kuti, ‘Anthu amene akutsatira Abisalomu agonjetsedwa.’