-
2 Samueli 17:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Tikawaukira kulikonse kumene ali, ndipo tikafika ngati mmene mame amagwera pansi. Sipakakhala opulumuka, kaya bambo anuwo kapena anthu onse amene ali nawo.
-