-
2 Samueli 17:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Ndiyeno mkazi wa munthuyo anatenga chinsalu nʼkuchiyala pamwamba pa chitsimepo, kenako anaunjikapo tirigu wosinja, ndipo palibe amene anadziwa chilichonse.
-