2 Samueli 17:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Anthuwo atachoka, Ahimazi ndi Yonatani anatuluka mʼchitsimemo nʼkupita kukauza Mfumu Davide kuti: “Nyamukani mwamsanga ndipo muwoloke mtsinje.” Kenako anawauza malangizo amene Ahitofeli anapereka.+
21 Anthuwo atachoka, Ahimazi ndi Yonatani anatuluka mʼchitsimemo nʼkupita kukauza Mfumu Davide kuti: “Nyamukani mwamsanga ndipo muwoloke mtsinje.” Kenako anawauza malangizo amene Ahitofeli anapereka.+