-
2 Samueli 18:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Nkhondoyi inafalikira dera lonselo. Komanso pa tsiku limeneli anthu amene anafera mʼnkhalango anali ambiri kuposa amene anaphedwa ndi lupanga.
-