2 Samueli 18:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno munthu wina anaona zimenezo nʼkupita kukauza Yowabu kuti:+ “Ndaona Abisalomu ali lende mumtengo waukulu.”
10 Ndiyeno munthu wina anaona zimenezo nʼkupita kukauza Yowabu kuti:+ “Ndaona Abisalomu ali lende mumtengo waukulu.”