-
2 Samueli 18:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Yowabu anafunsa munthuyo kuti: “Ngati wamuona, bwanji sunamuphe nthawi yomweyo? Ukanamupha, ndikanasangalala kwambiri ndipo ndikanakupatsa ndalama 10 zasiliva komanso lamba.”
-