2 Samueli 18:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma munthuyo anauza Yowabu kuti: “Ngakhale ndikanalandira ndalama 1,000 zasiliva, sindikanapha mwana wa mfumu. Paja tinamva mfumu ikukulamulani inuyo, Abisai ndi Itai kuti, ‘Aliyense asakaphe Abisalomu.’+
12 Koma munthuyo anauza Yowabu kuti: “Ngakhale ndikanalandira ndalama 1,000 zasiliva, sindikanapha mwana wa mfumu. Paja tinamva mfumu ikukulamulani inuyo, Abisai ndi Itai kuti, ‘Aliyense asakaphe Abisalomu.’+