2 Samueli 18:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndiyeno Yowabu anauza munthu wina wa ku Kusi* kuti:+ “Pita ukauze mfumu zimene waona.” Munthuyo anaweramira Yowabu nʼkuyamba kuthamanga.
21 Ndiyeno Yowabu anauza munthu wina wa ku Kusi* kuti:+ “Pita ukauze mfumu zimene waona.” Munthuyo anaweramira Yowabu nʼkuyamba kuthamanga.