-
2 Samueli 18:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Ahimazi mwana wa Zadoki anauzanso Yowabu kuti: “Kaya chichitike nʼchiyani, koma bwanji inenso ndithamange kutsatira munthu wa ku Kusi uja?” Koma Yowabu anati: “Mwana wanga, nʼchifukwa chiyani iwenso ukufuna kupita chonsecho palibe uthenga woti ukanene?”
-