-
2 Samueli 18:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Iye anaumirira nʼkunena kuti: “Kaya chichitike nʼchiyani, koma bwanji nanenso ndithamange?” Choncho Yowabu anati: “Thamanga!” Atatero Ahimazi anayamba kuthamanga kudutsa njira yakuchigawo cha Yorodano ndipo anamupitirira munthu wa ku Kusi uja.
-