-
2 Samueli 18:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 mlondayo anaonanso munthu wina akuthamanga. Ndiyeno mlondayo anafuula nʼkuuza mlonda wapageti kuti: “Munthu winanso akuthamanga, ali yekha.” Mfumu inati: “Ameneyunso akubweretsa uthenga.”
-