2 Samueli 18:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Kenako Ahimazi anauza mfumu kuti: “Zonse zili bwino!” Atatero anagwadira mfumuyo nʼkuwerama mpaka nkhope yake kufika pansi. Ndiyeno anati: “Atamandike Yehova Mulungu wanu, amene wapereka anthu amene anakuukirani inu mbuyanga mfumu!”+
28 Kenako Ahimazi anauza mfumu kuti: “Zonse zili bwino!” Atatero anagwadira mfumuyo nʼkuwerama mpaka nkhope yake kufika pansi. Ndiyeno anati: “Atamandike Yehova Mulungu wanu, amene wapereka anthu amene anakuukirani inu mbuyanga mfumu!”+