2 Samueli 18:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Koma mfumu inati: “Kodi mwana wanga Abisalomu ali bwino?” Ahimazi anayankha kuti: “Pamene Yowabu amatuma mtumiki wanu mfumu komanso ineyo, ndinaona chipwirikiti chachikulu, koma sindinadziwe kuti chikuchitika nʼchiyani.”+
29 Koma mfumu inati: “Kodi mwana wanga Abisalomu ali bwino?” Ahimazi anayankha kuti: “Pamene Yowabu amatuma mtumiki wanu mfumu komanso ineyo, ndinaona chipwirikiti chachikulu, koma sindinadziwe kuti chikuchitika nʼchiyani.”+