2 Samueli 18:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Kenako munthu wa ku Kusi uja anafika,+ ndipo ananena kuti: “Ndabweretsa uthenga mbuyanga mfumu. Lero Yehova wakuchitirani chilungamo pokulanditsani mʼmanja mwa anthu onse amene anakuukirani.”+
31 Kenako munthu wa ku Kusi uja anafika,+ ndipo ananena kuti: “Ndabweretsa uthenga mbuyanga mfumu. Lero Yehova wakuchitirani chilungamo pokulanditsani mʼmanja mwa anthu onse amene anakuukirani.”+