2 Samueli 18:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Koma mfumu inafunsa munthuyo kuti: “Kodi mwana wanga Abisalomu ali bwino?” Iye anayankha kuti: “Adani anu onse mbuyanga mfumu ndiponso anthu onse amene anakuukirani kuti akuchitireni zoipa, akhale ngati iyeyo.”+
32 Koma mfumu inafunsa munthuyo kuti: “Kodi mwana wanga Abisalomu ali bwino?” Iye anayankha kuti: “Adani anu onse mbuyanga mfumu ndiponso anthu onse amene anakuukirani kuti akuchitireni zoipa, akhale ngati iyeyo.”+