2 Samueli 19:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tsiku limenelo anthu analowa mumzinda mwakachetechete+ ngati anthu amene akuchita manyazi chifukwa choti athawa kunkhondo.
3 Tsiku limenelo anthu analowa mumzinda mwakachetechete+ ngati anthu amene akuchita manyazi chifukwa choti athawa kunkhondo.