2 Samueli 19:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako Yowabu anapita kunyumba ya mfumu nʼkuiuza kuti: “Lero mwachititsa manyazi atumiki anu onse amene apulumutsa moyo wanu, wa ana anu aamuna,+ ana anu aakazi,+ akazi anu komanso akazi anu aangʼono.*+
5 Kenako Yowabu anapita kunyumba ya mfumu nʼkuiuza kuti: “Lero mwachititsa manyazi atumiki anu onse amene apulumutsa moyo wanu, wa ana anu aamuna,+ ana anu aakazi,+ akazi anu komanso akazi anu aangʼono.*+