-
2 Samueli 19:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Mumakonda anthu amene amadana nanu ndipo mumadana ndi amene amakukondani. Lero mwasonyeza kuti atumiki anu ndi atsogoleri mulibe nawo ntchito ndipo sindikukayikira kuti Abisalomu akanakhala moyo koma ena tonsefe nʼkufa, simukanadandaula.
-