-
2 Samueli 19:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Ndiye nyamukani, mupite mukalimbikitse atumiki anu, chifukwa ngati simupita, ndithu ndikulumbira mʼdzina la Yehova, palibe munthu amene atsale ndi inu usiku uno. Zimenezi zikhala zoipa kwambiri kwa inu kuposa zoipa zonse zimene mwakumana nazo kuyambira muli mnyamata.”
-