2 Samueli 19:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiye Abisalomu amene tinamudzoza kuti akhale mtsogoleri wathu+ wafa kunkhondo.+ Nanga nʼchifukwa chiyani simukuchita chilichonse kuti mfumu ibwerere?”
10 Ndiye Abisalomu amene tinamudzoza kuti akhale mtsogoleri wathu+ wafa kunkhondo.+ Nanga nʼchifukwa chiyani simukuchita chilichonse kuti mfumu ibwerere?”