2 Samueli 19:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Inu ndinu abale anga ndipo ndife magazi amodzi.* Ndiye nʼchifukwa chiyani inu nokha simukuchita chilichonse kuti mfumu ibwerere?’
12 Inu ndinu abale anga ndipo ndife magazi amodzi.* Ndiye nʼchifukwa chiyani inu nokha simukuchita chilichonse kuti mfumu ibwerere?’