2 Samueli 19:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iye* atafika, anawolokera tsidya lina kuti akawolotse anthu a mʼbanja la mfumu komanso kuchita zilizonse zimene mfumuyo ingafune. Koma mfumu itatsala pangʼono kuwoloka Yorodano, Simeyi mwana wa Gera, anagwada pamaso pake.
18 Iye* atafika, anawolokera tsidya lina kuti akawolotse anthu a mʼbanja la mfumu komanso kuchita zilizonse zimene mfumuyo ingafune. Koma mfumu itatsala pangʼono kuwoloka Yorodano, Simeyi mwana wa Gera, anagwada pamaso pake.