2 Samueli 19:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiyeno anauza mfumu kuti: “Mbuyanga, mundikhululukire zimene ndinalakwitsa. Musakumbukire zoipa zimene ine mtumiki wanu+ ndinachita tsiku limene inu mbuyanga mfumu munkachoka ku Yerusalemu. Musasunge zimenezi mumtima mwanu mfumu.
19 Ndiyeno anauza mfumu kuti: “Mbuyanga, mundikhululukire zimene ndinalakwitsa. Musakumbukire zoipa zimene ine mtumiki wanu+ ndinachita tsiku limene inu mbuyanga mfumu munkachoka ku Yerusalemu. Musasunge zimenezi mumtima mwanu mfumu.