2 Samueli 19:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Nthawi yomweyo Abisai+ mwana wa Zeruya anati:+ “Pa zimene wanenazi, kodi Simeyi sakuyenera kuphedwa chifukwa choti anatemberera wodzozedwa wa Yehova?”+
21 Nthawi yomweyo Abisai+ mwana wa Zeruya anati:+ “Pa zimene wanenazi, kodi Simeyi sakuyenera kuphedwa chifukwa choti anatemberera wodzozedwa wa Yehova?”+