2 Samueli 19:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma Davide anati: “Chikukukhudzani nʼchiyani inu ana a Zeruya+ kuti lero muzitsutsana ndi ine? Kodi mu Isiraeli muyenera kuphedwa munthu lero? Kodi ine sindikudziwa kuti lero ndine mfumu ya Isiraeli?”
22 Koma Davide anati: “Chikukukhudzani nʼchiyani inu ana a Zeruya+ kuti lero muzitsutsana ndi ine? Kodi mu Isiraeli muyenera kuphedwa munthu lero? Kodi ine sindikudziwa kuti lero ndine mfumu ya Isiraeli?”