2 Samueli 19:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Atafika* ku Yerusalemu kukakumana ndi mfumu, mfumuyo inamufunsa kuti: “Mefiboseti, nʼchifukwa chiyani sunapite nane?”
25 Atafika* ku Yerusalemu kukakumana ndi mfumu, mfumuyo inamufunsa kuti: “Mefiboseti, nʼchifukwa chiyani sunapite nane?”