-
2 Samueli 19:30Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
30 Mefiboseti anayankha mfumu kuti: “Musiyeni atenge malo onsewo, kwa ine zili bwino chifukwa inu mbuyanga mfumu mwabwerera kunyumba yanu mwamtendere.”
-