2 Samueli 19:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ndiyeno mfumu inauza Barizilai kuti: “Tiyeni tiwoloke limodzi tipite ku Yerusalemu ndipo ndizikakupatsani chakudya.”+ 2 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:33 Nsanja ya Olonda,7/15/2007, tsa. 14
33 Ndiyeno mfumu inauza Barizilai kuti: “Tiyeni tiwoloke limodzi tipite ku Yerusalemu ndipo ndizikakupatsani chakudya.”+