-
2 Samueli 19:38Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
38 Mfumu inati: “Chimamu ndipita naye limodzi, ndipo ine ndikamuchitira zimene mukuona kuti nʼzabwino. Chilichonse chimene mudzapemphe kuti ndikuchitireni, ndidzakuchitirani.”
-