2 Samueli 19:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Pamene mfumu inkawoloka kupita ku Giligala,+ Chimamu anapita nawo. Ayuda onse komanso hafu ya anthu a ku Isiraeli anaperekeza mfumu.+
40 Pamene mfumu inkawoloka kupita ku Giligala,+ Chimamu anapita nawo. Ayuda onse komanso hafu ya anthu a ku Isiraeli anaperekeza mfumu.+