2 Samueli 20:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Zitatero, anthu onse a Isiraeli anachoka kwa Davide nʼkuyamba kutsatira Sheba mwana wa Bikiri.+ Koma anthu a ku Yuda, kuyambira ku Yorodano mpaka ku Yerusalemu, anakhalabe ndi mfumu yawo.+
2 Zitatero, anthu onse a Isiraeli anachoka kwa Davide nʼkuyamba kutsatira Sheba mwana wa Bikiri.+ Koma anthu a ku Yuda, kuyambira ku Yorodano mpaka ku Yerusalemu, anakhalabe ndi mfumu yawo.+