2 Samueli 21:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndiyeno mʼmasiku a Davide kunagwa njala+ kwa zaka zitatu zotsatizana. Choncho Davide anafunsa Yehova ndipo Yehova anamuuza kuti: “Sauli ndi anthu amʼnyumba yake ali ndi mlandu wa magazi chifukwa Sauli anapha Agibiyoni.”+
21 Ndiyeno mʼmasiku a Davide kunagwa njala+ kwa zaka zitatu zotsatizana. Choncho Davide anafunsa Yehova ndipo Yehova anamuuza kuti: “Sauli ndi anthu amʼnyumba yake ali ndi mlandu wa magazi chifukwa Sauli anapha Agibiyoni.”+