2 Samueli 21:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Agibiyoni anayankha kuti: “Sitikufuna siliva kapena golide+ pa nkhani ya Sauli ndi anthu amʼnyumba yake, komanso sitingaphe munthu aliyense mu Isiraeli.” Ndiyeno Davide anati: “Chilichonse chimene mungafune ndikuchitirani.”
4 Agibiyoni anayankha kuti: “Sitikufuna siliva kapena golide+ pa nkhani ya Sauli ndi anthu amʼnyumba yake, komanso sitingaphe munthu aliyense mu Isiraeli.” Ndiyeno Davide anati: “Chilichonse chimene mungafune ndikuchitirani.”