2 Samueli 21:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iye anawapereka kwa Agibiyoni ndipo Agibiyoniwo anapachika mitembo yawo paphiri kuti Yehova+ aone moti onse 7 anafera limodzi. Iwo anaphedwa mʼmasiku oyambirira a nthawi yokolola, kumayambiriro kwa nthawi yokolola balere. 2 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:9 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),3/2022, tsa. 13
9 Iye anawapereka kwa Agibiyoni ndipo Agibiyoniwo anapachika mitembo yawo paphiri kuti Yehova+ aone moti onse 7 anafera limodzi. Iwo anaphedwa mʼmasiku oyambirira a nthawi yokolola, kumayambiriro kwa nthawi yokolola balere.