2 Samueli 21:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Davide anauzidwa zimene Rizipa mwana wa Aya, mkazi wamngʼono* wa Sauli anachita.