2 Samueli 21:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iye anabweretsa mafupa a Sauli ndi a mwana wake Yonatani. Atatero anasonkhanitsanso mafupa a anthu amene anaphedwa* aja.+
13 Iye anabweretsa mafupa a Sauli ndi a mwana wake Yonatani. Atatero anasonkhanitsanso mafupa a anthu amene anaphedwa* aja.+