2 Samueli 22:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mulungu wanga ndi thanthwe langa,+ ine ndimathawira kwa iye,Iye ndi chishango changa,+ nyanga* yanga ya chipulumutso* ndi malo anga achitetezo.*+Komanso ndi malo anga othawirako,+ mpulumutsi wanga+ amene amandipulumutsa kwa anthu achiwawa.
3 Mulungu wanga ndi thanthwe langa,+ ine ndimathawira kwa iye,Iye ndi chishango changa,+ nyanga* yanga ya chipulumutso* ndi malo anga achitetezo.*+Komanso ndi malo anga othawirako,+ mpulumutsi wanga+ amene amandipulumutsa kwa anthu achiwawa.