-
2 Samueli 22:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Ndimapempha Yehova, amene ndi woyenera kutamandidwa, kuti andithandize.
Ndipo adzandipulumutsa kwa adani anga.
-
4 Ndimapempha Yehova, amene ndi woyenera kutamandidwa, kuti andithandize.
Ndipo adzandipulumutsa kwa adani anga.