2 Samueli 22:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Utsi unatuluka mʼmphuno mwake,Ndipo moto wowononga unatuluka mʼkamwa mwake;+Makala oyaka anatuluka mwa iye.
9 Utsi unatuluka mʼmphuno mwake,Ndipo moto wowononga unatuluka mʼkamwa mwake;+Makala oyaka anatuluka mwa iye.