2 Samueli 22:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kenako anaika mdima momuzungulira ngati tenti,+Mʼmadzi akuda ndi mʼmitambo yakuda.