2 Samueli 22:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Anatambasula dzanja lake kuchokera kumwamba;Anandigwira nʼkundivuula mʼmadzi akuya.+