2 Samueli 22:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Anandipulumutsa kwa mdani wanga wamphamvu,+Kwa anthu odana nane amene anali amphamvu kuposa ine.