2 Samueli 22:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Yehova amandidalitsa mogwirizana ndi chilungamo changa;+Amandipatsa mphoto mogwirizana ndi manja anga osalakwa.*+
21 Yehova amandidalitsa mogwirizana ndi chilungamo changa;+Amandipatsa mphoto mogwirizana ndi manja anga osalakwa.*+