2 Samueli 22:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Inu Yehova ndinu nyale yanga;+Yehova ndi amene amandiunikira mumdima.+