2 Samueli 22:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Mumakulitsa njira kuti mapazi anga azidutsamo,Ndipo mapazi anga sadzaterereka.+