2 Samueli 22:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Mudzandipatsa mphamvu kuti ndithe kumenya nkhondo;+Mudzachititsa kuti adani anga agonje.+